17 Poyankha Yesu anati: “Inu a m’badwo wopanda chikhulupiriro ndi wopotoka maganizo,+ kodi ndikhala nanube mpaka liti? Ndipitirize kukupirirani mpaka liti? Bwera nayeni kuno.”
41 Poyankha Yesu anati: “Inu a m’badwo+ wopanda chikhulupiriro ndi wopotoka maganizo, kodi ndikhala nanube ndi kupitiriza kukupirirani mpaka liti? Bwera naye kuno mwana wakoyo.”+