Yobu 1:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndiyeno Yehova anafunsanso Satana kuti: “Kodi mtima wako uli pa mtumiki wanga Yobu, poti palibe wina wokhala ngati iyeyo padziko lapansi?+ Iyetu ndi munthu wopanda cholakwa+ ndi wowongoka mtima,+ woopa Mulungu+ ndi wopewa zoipa.”+ Yobu 1:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pamenepo Satana anamuyankha Yehova kuti: “Kodi mukuganiza kuti Yobu amangoopa Mulungu pachabe?+ Salimo 127:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Wodala ndi mwamuna wamphamvu amene wadzaza+ kachikwama kake ka mivi ndi mivi imeneyo.Abambo oterowo sadzachita manyazi,+Pakuti anawo adzalankhula ndi adani pachipata.
8 Ndiyeno Yehova anafunsanso Satana kuti: “Kodi mtima wako uli pa mtumiki wanga Yobu, poti palibe wina wokhala ngati iyeyo padziko lapansi?+ Iyetu ndi munthu wopanda cholakwa+ ndi wowongoka mtima,+ woopa Mulungu+ ndi wopewa zoipa.”+
5 Wodala ndi mwamuna wamphamvu amene wadzaza+ kachikwama kake ka mivi ndi mivi imeneyo.Abambo oterowo sadzachita manyazi,+Pakuti anawo adzalankhula ndi adani pachipata.