Numeri 12:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Moseyo anali munthu wofatsa kwambiri+ kuposa anthu onse amene anali padziko lapansi. Miyambo 14:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Mfumu imasangalala ndi wantchito wochita zinthu mozindikira,+ koma imakwiya ndi wantchito wochita zinthu zochititsa manyazi.+
35 Mfumu imasangalala ndi wantchito wochita zinthu mozindikira,+ koma imakwiya ndi wantchito wochita zinthu zochititsa manyazi.+