Salimo 147:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Yehova amathandiza anthu ofatsa,+Koma anthu oipa amawagwetsera pansi.+ Salimo 149:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pakuti Yehova amasangalala ndi anthu ake.+Iye amakongoletsa anthu ofatsa ndi chipulumutso.+ Mateyu 11:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Senzani goli+ langa ndipo phunzirani kwa ine,+ chifukwa ndine wofatsa+ ndi wodzichepetsa, ndipo mudzatsitsimulidwa,+ Mateyu 21:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 “Uzani mwana wamkazi wa Ziyoni kuti, ‘Taona! Mfumu yako ikubwera kwa iwe.+ Ndi yofatsa+ ndipo yakwera bulu wamng’ono wamphongo, mwana wa nyama yonyamula katundu.’”+ 1 Petulo 3:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Koma kukhale kwa munthu wobisika+ wamumtima, atavala zovala zosawonongeka,+ ndizo mzimu wabata ndi wofatsa+ umene uli wamtengo wapatali pamaso pa Mulungu.
29 Senzani goli+ langa ndipo phunzirani kwa ine,+ chifukwa ndine wofatsa+ ndi wodzichepetsa, ndipo mudzatsitsimulidwa,+
5 “Uzani mwana wamkazi wa Ziyoni kuti, ‘Taona! Mfumu yako ikubwera kwa iwe.+ Ndi yofatsa+ ndipo yakwera bulu wamng’ono wamphongo, mwana wa nyama yonyamula katundu.’”+
4 Koma kukhale kwa munthu wobisika+ wamumtima, atavala zovala zosawonongeka,+ ndizo mzimu wabata ndi wofatsa+ umene uli wamtengo wapatali pamaso pa Mulungu.