Numeri 12:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Moseyo anali munthu wofatsa kwambiri+ kuposa anthu onse amene anali padziko lapansi. Salimo 37:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Koma anthu ofatsa adzalandira dziko lapansi,+Ndipo adzasangalala ndi mtendere wochuluka.+ Salimo 146:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Yehova amatsegula maso a anthu akhungu.+Yehova amaweramutsa anthu owerama chifukwa cha masautso.+Yehova amakonda anthu olungama.+
8 Yehova amatsegula maso a anthu akhungu.+Yehova amaweramutsa anthu owerama chifukwa cha masautso.+Yehova amakonda anthu olungama.+