Salimo 145:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Yehova amachirikiza amene ali pafupi kugwa,+Ndipo amaweramutsa onse amene awerama chifukwa cha masautso.+ Salimo 147:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Yehova amathandiza anthu ofatsa,+Koma anthu oipa amawagwetsera pansi.+ Luka 13:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pamenepo anaika manja ake pamayiyo, ndipo nthawi yomweyo anaweramuka,+ n’kuyamba kutamanda Mulungu. 2 Akorinto 7:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Komabe Mulungu, amene amalimbikitsa+ osautsika mtima, anatilimbikitsa ndi kukhalapo* kwa Tito.
14 Yehova amachirikiza amene ali pafupi kugwa,+Ndipo amaweramutsa onse amene awerama chifukwa cha masautso.+
13 Pamenepo anaika manja ake pamayiyo, ndipo nthawi yomweyo anaweramuka,+ n’kuyamba kutamanda Mulungu.