Aroma 7:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Mumtima mwanga+ ndimasangalala kwambiri+ ndi chilamulo cha Mulungu, Aefeso 3:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Kutinso mogwirizana ndi chuma+ cha ulemerero wake, akuloleni kuti munthu wanu wamkati+ akhale wamphamvu, mwa mphamvu ya mzimu wake,+
16 Kutinso mogwirizana ndi chuma+ cha ulemerero wake, akuloleni kuti munthu wanu wamkati+ akhale wamphamvu, mwa mphamvu ya mzimu wake,+