Salimo 35:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Onse amene amakonda chilungamo changa afuule mosangalala ndi kukondwera.+Nthawi zonse azinena kuti:+“Alemekezeke Yehova, amene amasangalala mtumiki wake akakhala pa mtendere.”+ Salimo 84:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pakuti Yehova Mulungu ndi dzuwa+ ndiponso chishango.+Iye amatikomera mtima ndi kutipatsa ulemerero.+Yehova samana anthu oyenda mosalakwa chinthu chilichonse chabwino.+
27 Onse amene amakonda chilungamo changa afuule mosangalala ndi kukondwera.+Nthawi zonse azinena kuti:+“Alemekezeke Yehova, amene amasangalala mtumiki wake akakhala pa mtendere.”+
11 Pakuti Yehova Mulungu ndi dzuwa+ ndiponso chishango.+Iye amatikomera mtima ndi kutipatsa ulemerero.+Yehova samana anthu oyenda mosalakwa chinthu chilichonse chabwino.+