Salimo 27:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Yehova ndiye kuwala+ kwanga ndi chipulumutso changa.+Ndingaopenso ndani?+Yehova ndiye malo a chitetezo cha moyo wanga.+Ndingachitenso mantha ndi ndani?+ Yesaya 60:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Dzuwa silidzakhalanso lokuunikira masana, ndipo mwezi sudzakuunikiranso. Kwa iwe, Yehova adzakhala kuwala kosatha mpaka kalekale,+ ndipo Mulungu wako adzakhala kukongola kwako.+
27 Yehova ndiye kuwala+ kwanga ndi chipulumutso changa.+Ndingaopenso ndani?+Yehova ndiye malo a chitetezo cha moyo wanga.+Ndingachitenso mantha ndi ndani?+
19 Dzuwa silidzakhalanso lokuunikira masana, ndipo mwezi sudzakuunikiranso. Kwa iwe, Yehova adzakhala kuwala kosatha mpaka kalekale,+ ndipo Mulungu wako adzakhala kukongola kwako.+