Salimo 62:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Chipulumutso ndi ulemerero wanga zili mwa Mulungu.+Iye ndi thanthwe langa lolimba ndi malo anga othawirako.+ Salimo 71:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 M’kamwa mwanga mwadzaza mawu otamanda inu,+Ndipo pakamwa panga pakunena za ulemerero wanu tsiku lonse.+ Zekariya 2:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ine ndidzamuzungulira ngati mpanda wake wamoto+ ndipo ndidzamudzaza ndi ulemerero wanga,”’ watero Yehova.”+ Luka 2:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Maso anga aona kuwala+ kochotsa nsalu yophimba+ mitundu ya anthu+ ndi ulemerero wa anthu anu Aisiraeli.”
7 Chipulumutso ndi ulemerero wanga zili mwa Mulungu.+Iye ndi thanthwe langa lolimba ndi malo anga othawirako.+
8 M’kamwa mwanga mwadzaza mawu otamanda inu,+Ndipo pakamwa panga pakunena za ulemerero wanu tsiku lonse.+
5 Ine ndidzamuzungulira ngati mpanda wake wamoto+ ndipo ndidzamudzaza ndi ulemerero wanga,”’ watero Yehova.”+
32 Maso anga aona kuwala+ kochotsa nsalu yophimba+ mitundu ya anthu+ ndi ulemerero wa anthu anu Aisiraeli.”