Aroma 12:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Sangalalani ndi anthu amene akusangalala.+ Lirani ndi anthu amene akulira. 1 Akorinto 12:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Ndipo chiwalo chimodzi chikavutika, ziwalo zina zonse zimavutikira nacho limodzi,+ komanso chiwalo chimodzi chikalemekezedwa,+ ziwalo zina zonse zimasangalalira nacho limodzi.+
26 Ndipo chiwalo chimodzi chikavutika, ziwalo zina zonse zimavutikira nacho limodzi,+ komanso chiwalo chimodzi chikalemekezedwa,+ ziwalo zina zonse zimasangalalira nacho limodzi.+