Salimo 70:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Onse amene akufunafuna inu akondwere ndi kusangalala mwa inu,+Ndipo onse amene amakonda chipulumutso chanu, nthawi zonse azinena kuti: “Mulungu alemekezeke!”+
4 Onse amene akufunafuna inu akondwere ndi kusangalala mwa inu,+Ndipo onse amene amakonda chipulumutso chanu, nthawi zonse azinena kuti: “Mulungu alemekezeke!”+