Genesis 50:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Yosefe anakhalabe ndi moyo mpaka kuona ana a Efuraimu a m’badwo wachitatu.+ Anaonanso ana a Makiri+ mwana wa Manase. Onsewo anabadwira pamiyendo pa Yosefe.+ Yobu 1:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Yobu anali ndi ana aamuna 7, ndi ana aakazi atatu.+ Yobu 42:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Anakhalanso ndi ana aamuna 7 ndi ana aakazi atatu.+
23 Yosefe anakhalabe ndi moyo mpaka kuona ana a Efuraimu a m’badwo wachitatu.+ Anaonanso ana a Makiri+ mwana wa Manase. Onsewo anabadwira pamiyendo pa Yosefe.+