Nehemiya 5:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Abwanamkubwa amene analipo ine ndisanakhale, ankalemetsa anthu, ndipo tsiku ndi tsiku anali kulandira masekeli* 40 a siliva kuti akagule chakudya ndi vinyo. Komanso atumiki awo anali kupondereza anthu.+ Koma ine sindinachite zimenezo+ chifukwa choopa Mulungu.+ Salimo 19:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kuopa+ Yehova n’koyera, ndipo kudzakhalapo kwamuyaya.Zigamulo+ za Yehova n’zolondola,+ ndipo pa mbali iliyonse zasonyezadi kuti ndi zolungama.+ Mlaliki 12:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Poti zonse zanenedwa, mfundo yaikulu ndi yakuti: Opa Mulungu woona+ ndi kusunga malamulo ake+ chifukwa zimenezi ndiye zimene munthu ayenera kuchita.
15 Abwanamkubwa amene analipo ine ndisanakhale, ankalemetsa anthu, ndipo tsiku ndi tsiku anali kulandira masekeli* 40 a siliva kuti akagule chakudya ndi vinyo. Komanso atumiki awo anali kupondereza anthu.+ Koma ine sindinachite zimenezo+ chifukwa choopa Mulungu.+
9 Kuopa+ Yehova n’koyera, ndipo kudzakhalapo kwamuyaya.Zigamulo+ za Yehova n’zolondola,+ ndipo pa mbali iliyonse zasonyezadi kuti ndi zolungama.+
13 Poti zonse zanenedwa, mfundo yaikulu ndi yakuti: Opa Mulungu woona+ ndi kusunga malamulo ake+ chifukwa zimenezi ndiye zimene munthu ayenera kuchita.