Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Nehemiya 5:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Ndiyeno ndinati: “Zimene mukuchitazi si zabwino ayi.+ Kodi simuyenera kuyenda moopa+ Mulungu+ kuti tipewe chitonzo+ cha adani athu, anthu a mitundu ina?+

  • Salimo 112:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 112 Tamandani Ya, anthu inu!+

      א [ʼAʹleph]

      Wodala ndi munthu woopa Yehova,+

      ב [Behth]

      Munthu amene amasangalala kwambiri+ ndi malamulo ake.+

  • Salimo 147:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Yehova amasangalala ndi anthu amene amamuopa,+

      Amene amayembekezera kukoma mtima kwake kosatha.+

  • Miyambo 16:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Cholakwa chimaphimbika ndi kukoma mtima kosatha ndiponso choonadi,+ ndipo chifukwa choopa Yehova munthu amapatuka pa choipa.+

  • Mlaliki 12:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Poti zonse zanenedwa, mfundo yaikulu ndi yakuti: Opa Mulungu woona+ ndi kusunga malamulo ake+ chifukwa zimenezi ndiye zimene munthu ayenera kuchita.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena