1 Samueli 2:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Musatero+ ana anga, chifukwa nkhani imene ndikumva, imene anthu a Yehova akufalitsa, si yabwino ayi.+ Yesaya 58:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndimafunanso kuti muzigawira chakudya chanu anthu anjala,+ ndiponso kuti muziitanira m’nyumba zanu anthu osautsika ndi osowa pokhala.+ Ndimafuna kuti mukaona munthu wosavala muzimuveka+ ndiponso kuti musamadzibise kwa abale anu.+
24 Musatero+ ana anga, chifukwa nkhani imene ndikumva, imene anthu a Yehova akufalitsa, si yabwino ayi.+
7 Ndimafunanso kuti muzigawira chakudya chanu anthu anjala,+ ndiponso kuti muziitanira m’nyumba zanu anthu osautsika ndi osowa pokhala.+ Ndimafuna kuti mukaona munthu wosavala muzimuveka+ ndiponso kuti musamadzibise kwa abale anu.+