Ekisodo 15:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mphamvu ndi nyonga yanga ndi Ya,*+ pakuti wandipulumutsa.+Ameneyu ndi Mulungu wanga, ndidzam’tamanda.+ Ndiye Mulungu wa atate anga,+ ndidzam’kweza.+ Salimo 117:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pakuti kukoma mtima kosatha kumene watisonyeza ndi kwakukulu.+Ndipo choonadi+ cha Yehova chidzakhalapobe mpaka kalekale.Tamandani Ya, anthu inu!+ Salimo 150:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Chopuma chilichonse chitamande Ya.+Tamandani Ya, anthu inu!+ Chivumbulutso 19:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Zimenezi zitatha, ndinamva mawu ofuula kumwamba+ ngati mawu a khamu lalikulu, akuti: “Tamandani Ya,* anthu inu!+ Chipulumutso,+ ulemerero, ndi mphamvu ndi za Mulungu wathu,+
2 Mphamvu ndi nyonga yanga ndi Ya,*+ pakuti wandipulumutsa.+Ameneyu ndi Mulungu wanga, ndidzam’tamanda.+ Ndiye Mulungu wa atate anga,+ ndidzam’kweza.+
2 Pakuti kukoma mtima kosatha kumene watisonyeza ndi kwakukulu.+Ndipo choonadi+ cha Yehova chidzakhalapobe mpaka kalekale.Tamandani Ya, anthu inu!+
19 Zimenezi zitatha, ndinamva mawu ofuula kumwamba+ ngati mawu a khamu lalikulu, akuti: “Tamandani Ya,* anthu inu!+ Chipulumutso,+ ulemerero, ndi mphamvu ndi za Mulungu wathu,+