Salimo 112:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 112 Tamandani Ya, anthu inu!+ א [ʼAʹleph]Wodala ndi munthu woopa Yehova,+ב [Behth]Munthu amene amasangalala kwambiri+ ndi malamulo ake.+ Salimo 148:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Iye adzakweza nyanga* ya anthu ake.+Adzachititsa kuti anthu ake onse okhulupirika atamandike,+Amene ndi ana a Isiraeli, anthu amene ali pafupi ndi iye.+Tamandani Ya, anthu inu!+ Chivumbulutso 19:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Nthawi yomweyo, ananenanso kachiwiri kuti: “Tamandani Ya, anthu inu!+ Utsi wochokera kwa iye udzafuka kwamuyaya.”+
112 Tamandani Ya, anthu inu!+ א [ʼAʹleph]Wodala ndi munthu woopa Yehova,+ב [Behth]Munthu amene amasangalala kwambiri+ ndi malamulo ake.+
14 Iye adzakweza nyanga* ya anthu ake.+Adzachititsa kuti anthu ake onse okhulupirika atamandike,+Amene ndi ana a Isiraeli, anthu amene ali pafupi ndi iye.+Tamandani Ya, anthu inu!+
3 Nthawi yomweyo, ananenanso kachiwiri kuti: “Tamandani Ya, anthu inu!+ Utsi wochokera kwa iye udzafuka kwamuyaya.”+