Ekisodo 19:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Tsopano ngati mudzalabadiradi+ mawu anga ndi kusunga pangano langa,+ pamenepo mudzakhaladi chuma changa chapadera pakati pa anthu ena onse,+ chifukwa dziko lonse lapansi ndi langa.+ Aefeso 2:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Chotero iye anabwera n’kulengeza uthenga wabwino wa mtendere+ kwa inuyo, inu akutali, ndipo analengezanso mtendere kwa apafupi,+
5 Tsopano ngati mudzalabadiradi+ mawu anga ndi kusunga pangano langa,+ pamenepo mudzakhaladi chuma changa chapadera pakati pa anthu ena onse,+ chifukwa dziko lonse lapansi ndi langa.+
17 Chotero iye anabwera n’kulengeza uthenga wabwino wa mtendere+ kwa inuyo, inu akutali, ndipo analengezanso mtendere kwa apafupi,+