Salimo 119:160 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 160 Mawu anu onse ndi choonadi chokhachokha,+Ndipo chigamulo chanu chilichonse cholungama chidzakhalapo mpaka kalekale.+ Chivumbulutso 16:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kenako ndinamva guwa lansembe likunena kuti: “Inde, Yehova Mulungu, inu Wamphamvuyonse,+ zigamulo zanu n’zoona ndi zolungama.”+
160 Mawu anu onse ndi choonadi chokhachokha,+Ndipo chigamulo chanu chilichonse cholungama chidzakhalapo mpaka kalekale.+
7 Kenako ndinamva guwa lansembe likunena kuti: “Inde, Yehova Mulungu, inu Wamphamvuyonse,+ zigamulo zanu n’zoona ndi zolungama.”+