Genesis 6:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Tsopano nayi mbiri ya Nowa. Nowa anali munthu wolungama.+ Iye anali wopanda cholakwa pakati pa anthu a m’nthawi yake. Nowa anayenda ndi Mulungu woona.+ Salimo 37:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Ona munthu wosalakwa ndipo yang’anitsitsa munthu wolungama,+Pakuti tsogolo la munthu ameneyu ndi lamtendere.+ Yohane 1:47 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 47 Yesu ataona Natanayeli akubwera momulunjika anati: “Onani Mwisiraeli ndithu, amene mwa iye mulibe chinyengo.”+
9 Tsopano nayi mbiri ya Nowa. Nowa anali munthu wolungama.+ Iye anali wopanda cholakwa pakati pa anthu a m’nthawi yake. Nowa anayenda ndi Mulungu woona.+
37 Ona munthu wosalakwa ndipo yang’anitsitsa munthu wolungama,+Pakuti tsogolo la munthu ameneyu ndi lamtendere.+
47 Yesu ataona Natanayeli akubwera momulunjika anati: “Onani Mwisiraeli ndithu, amene mwa iye mulibe chinyengo.”+