Yobu 42:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Yehova anadalitsa+ kwambiri mapeto a Yobu kuposa chiyambi chake+ moti iye anakhala ndi nkhosa 14,000, ngamila 6,000, ng’ombe 2,000 zimene zinkagwira ntchito zili ziwiriziwiri, ndi abulu aakazi 1,000. Yobu 42:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Pambuyo pa zimenezi, Yobu anakhala ndi moyo zaka 140+ ndipo anaona ana ake ndi zidzukulu zake+ mpaka m’badwo wachinayi. Miyambo 28:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Munthu amene amasocheretsa anthu owongoka mtima+ kuti ayende m’njira yoipa, adzagwera m’dzenje lake lomwe.+ Koma anthu osalakwa adzapeza zabwino.+ Yesaya 32:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Anthu anga adzakhala pamalo amtendere ndi pamalo otetezeka. Adzakhala m’malo abata ndiponso aphee!+
12 Yehova anadalitsa+ kwambiri mapeto a Yobu kuposa chiyambi chake+ moti iye anakhala ndi nkhosa 14,000, ngamila 6,000, ng’ombe 2,000 zimene zinkagwira ntchito zili ziwiriziwiri, ndi abulu aakazi 1,000.
16 Pambuyo pa zimenezi, Yobu anakhala ndi moyo zaka 140+ ndipo anaona ana ake ndi zidzukulu zake+ mpaka m’badwo wachinayi.
10 Munthu amene amasocheretsa anthu owongoka mtima+ kuti ayende m’njira yoipa, adzagwera m’dzenje lake lomwe.+ Koma anthu osalakwa adzapeza zabwino.+
18 Anthu anga adzakhala pamalo amtendere ndi pamalo otetezeka. Adzakhala m’malo abata ndiponso aphee!+