Miyambo 27:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mwana wanga, khala wanzeru ndi kukondweretsa mtima wanga,+ kuti ndimuyankhe amene akunditonza.+