Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 15:30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 “‘Koma munthu amene wachita cholakwa mwadala,+ kaya akhale mbadwa kapena mlendo, kumene kuli kunyoza Yehova,+ munthuyo aphedwe kuti asakhalenso pakati pa anthu ake.+

  • 1 Samueli 2:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Tsopano ana aamuna a Eli anali anthu opanda pake.+ Iwo anali kunyalanyaza Yehova.+

  • 1 Samueli 2:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Tchimo la atumikiwa linakula kwambiri pamaso pa Yehova,+ chifukwa amuna amenewa sanali kulemekeza nsembe ya Yehova.+

  • 1 Samueli 2:30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 “‘N’chifukwa chake Yehova Mulungu wa Isiraeli wanena kuti: “Ndinanenadi kuti, A m’nyumba yako ndiponso a m’nyumba ya kholo lako adzanditumikira mpaka kalekale.”+ Koma tsopano Yehova akuti: “Sindingachitenso zimenezo, chifukwa amene akundilemekeza+ ndiwalemekeza,+ koma amene akundinyoza ndi opanda pake kwa ine.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena