-
1 Samueli 2:30Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
30 Nʼchifukwa chake Yehova Mulungu wa Isiraeli wanena kuti: “Ndinanenadi kuti a mʼbanja lako ndiponso a mʼbanja la kholo lako adzanditumikira mpaka kalekale.”+ Koma tsopano Yehova akuti: “Sindingachitenso zimenezo, chifukwa amene akundilemekeza ndidzawalemekeza+ koma amene akundinyoza, adzanyozedwa.”
-