Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 28:45
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 45 “Matemberero onsewa+ adzakugwera, kukutsatira ndi kukupeza kufikira utafafanizika,+ chifukwa sunamvere mawu a Yehova Mulungu wako mwa kusunga malamulo ndi mfundo zake zimene anakupatsa.+

  • 2 Mafumu 2:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Pomalizira pake Elisa anatembenuka ndipo anawaona. Atatero anawaitanira tsoka+ m’dzina la Yehova. Kenako zimbalangondo ziwiri zazikazi+ zinatuluka m’thengo n’kukhadzulapo anyamata 42.+

  • Ezekieli 18:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 “‘Munthu wolungama akasiya chilungamo chake n’kumachita zinthu zopanda chilungamo,+ akamachita zopanda chilungamo+ n’kumakhalabe ndi moyo, zinthu zolungama zonse zimene anachita sizidzakumbukiridwa.+ Iye adzafa chifukwa chochita zinthu mosakhulupirika ndiponso chifukwa cha machimo ake amene anachita.+

  • Malaki 2:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 “Inenso ndidzachititsa kuti inu mukhale anthu onyozeka ndi otsika kwa anthu onse,+ chifukwa simunayende m’njira zanga, koma munali kukondera pa nkhani zokhudza chilamulo.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena