Aheberi 10:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 “Koma wolungama wanga adzakhala ndi moyo mwa chikhulupiriro chake,”+ ndipo “ngati wabwerera m’mbuyo, ine sindikondwera naye.”+ 2 Yohane 8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Samalani kuti musalephere kulandira mphoto ya zinthu zimene tazigwirira kale ntchito, kuti mudzalandire mphoto yokwanira.+
38 “Koma wolungama wanga adzakhala ndi moyo mwa chikhulupiriro chake,”+ ndipo “ngati wabwerera m’mbuyo, ine sindikondwera naye.”+
8 Samalani kuti musalephere kulandira mphoto ya zinthu zimene tazigwirira kale ntchito, kuti mudzalandire mphoto yokwanira.+