Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 15:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 “Ndikumva chisoni+ kuti ndinaika Sauli kukhala mfumu. Iye watembenuka,+ wasiya kunditsatira, ndipo sakumvera mawu anga.”+ Samueli anavutika maganizo kwambiri ndi nkhani imeneyi+ moti anafuulira Yehova usiku wonse.+

  • 1 Mafumu 11:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Pamene iye anali kukalamba,+ akazi ake anali atapotoza+ mtima wake moti iye anali kutsatira milungu ina.+ Sanatumikire Yehova Mulungu wake ndi mtima wathunthu+ monga mmene anachitira Davide bambo ake.

  • Ezekieli 33:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 “Iwe mwana wa munthu, uza anthu a mtundu wako kuti, ‘Munthu wolungama akapanduka, chilungamo chake sichidzamupulumutsa pa tsiku la kupanduka kwake.+ Koma munthu woipa akabwerera n’kusiya zoipa zakezo, sadzafa chifukwa cha zoipazo pa tsiku limene adzabwerere n’kuzisiya.+ Komanso munthu wolungama sadzakhalabe ndi moyo chifukwa cha chilungamo chake pa tsiku limene adzachimwe.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena