Salimo 36:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pakuti amadzinyenga yekha,+Ndipo sazindikira cholakwa chake ndi kudana nacho.+ Salimo 125:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Koma anthu obwerera kunjira zawo zokhotakhota,+Yehova adzawapereka ku chilango pamodzi ndi ochita zopweteka anzawo.+Ndipo mu Isiraeli mudzakhala mtendere.+ Mlaliki 4:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Mwana wosauka koma wanzeru ali bwino+ kuposa mfumu yokalamba koma yopusa,+ imene sionanso kufunika kochenjezedwa.+ Malaki 3:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kuyambira m’masiku a makolo anu mwakhala mukupatuka pa malamulo anga ndipo simunawasunge.+ Bwererani kwa ine ndipo ine ndibwerera kwa inu,”+ watero Yehova wa makamu. Koma inu mukunena kuti: “Tibwerere motani?”
5 Koma anthu obwerera kunjira zawo zokhotakhota,+Yehova adzawapereka ku chilango pamodzi ndi ochita zopweteka anzawo.+Ndipo mu Isiraeli mudzakhala mtendere.+
13 Mwana wosauka koma wanzeru ali bwino+ kuposa mfumu yokalamba koma yopusa,+ imene sionanso kufunika kochenjezedwa.+
7 Kuyambira m’masiku a makolo anu mwakhala mukupatuka pa malamulo anga ndipo simunawasunge.+ Bwererani kwa ine ndipo ine ndibwerera kwa inu,”+ watero Yehova wa makamu. Koma inu mukunena kuti: “Tibwerere motani?”