Salimo 128:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndipo uone ana a ana ako.+Mtendere ukhale pa Isiraeli.+ Ezekieli 37:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 “‘“Ndidzachita nawo pangano la mtendere,+ moti adzakhala m’pangano limene lidzakhalepo mpaka kalekale.+ Ine ndidzawakhazikitsa m’dzikolo, ndidzawachulukitsa+ ndipo ndidzakhazikitsa malo anga opatulika pakati pawo mpaka kalekale.+ Agalatiya 6:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ndipo onse otsatira lamulo limeneli la mmene tiyenera kukhalira, amene ndi Isiraeli wa Mulungu, akhale ndi mtendere ndiponso chifundo.+
26 “‘“Ndidzachita nawo pangano la mtendere,+ moti adzakhala m’pangano limene lidzakhalepo mpaka kalekale.+ Ine ndidzawakhazikitsa m’dzikolo, ndidzawachulukitsa+ ndipo ndidzakhazikitsa malo anga opatulika pakati pawo mpaka kalekale.+
16 Ndipo onse otsatira lamulo limeneli la mmene tiyenera kukhalira, amene ndi Isiraeli wa Mulungu, akhale ndi mtendere ndiponso chifundo.+