Genesis 50:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Yosefe anakhalabe ndi moyo mpaka kuona ana a Efuraimu a m’badwo wachitatu.+ Anaonanso ana a Makiri+ mwana wa Manase. Onsewo anabadwira pamiyendo pa Yosefe.+ Yobu 42:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Pambuyo pa zimenezi, Yobu anakhala ndi moyo zaka 140+ ndipo anaona ana ake ndi zidzukulu zake+ mpaka m’badwo wachinayi.
23 Yosefe anakhalabe ndi moyo mpaka kuona ana a Efuraimu a m’badwo wachitatu.+ Anaonanso ana a Makiri+ mwana wa Manase. Onsewo anabadwira pamiyendo pa Yosefe.+
16 Pambuyo pa zimenezi, Yobu anakhala ndi moyo zaka 140+ ndipo anaona ana ake ndi zidzukulu zake+ mpaka m’badwo wachinayi.