Deuteronomo 4:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Pamapeto pake, mawu amenewa akadzakwaniritsidwa pa inu, n’kukhala pamavuto aakulu, mudzabwereradi kwa Yehova Mulungu wanu+ ndi kumvetsera mawu ake.+ Yeremiya 3:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pita, ndipo ukalengeze mawu awa kumpoto+ kuti: “‘Yehova wanena kuti: “Bwerera Isiraeli wopanduka iwe. Sindidzakuyang’anani mokwiya anthu inu+ pakuti ndine wokhulupirika,”+ watero Yehova.+ “Sindidzakhala wokwiya mpaka kalekale.+ Zekariya 1:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “Uwauze kuti, ‘Yehova wa makamu wanena kuti: “‘Bwererani kwa ine,’+ watero Yehova wa makamu, ‘ndipo ine ndidzabwerera kwa inu,’+ akutero Yehova wa makamu.”’ Yakobo 4:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Yandikirani Mulungu, ndipo iyenso adzakuyandikirani.+ Yeretsani manja anu ochimwa inu,+ ndipo yeretsani mitima yanu,+ okayikakayika inu.+
30 Pamapeto pake, mawu amenewa akadzakwaniritsidwa pa inu, n’kukhala pamavuto aakulu, mudzabwereradi kwa Yehova Mulungu wanu+ ndi kumvetsera mawu ake.+
12 Pita, ndipo ukalengeze mawu awa kumpoto+ kuti: “‘Yehova wanena kuti: “Bwerera Isiraeli wopanduka iwe. Sindidzakuyang’anani mokwiya anthu inu+ pakuti ndine wokhulupirika,”+ watero Yehova.+ “Sindidzakhala wokwiya mpaka kalekale.+
3 “Uwauze kuti, ‘Yehova wa makamu wanena kuti: “‘Bwererani kwa ine,’+ watero Yehova wa makamu, ‘ndipo ine ndidzabwerera kwa inu,’+ akutero Yehova wa makamu.”’
8 Yandikirani Mulungu, ndipo iyenso adzakuyandikirani.+ Yeretsani manja anu ochimwa inu,+ ndipo yeretsani mitima yanu,+ okayikakayika inu.+