Miyambo 19:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Wosauka amene akuyenda ndi mtima wosagawanika ali bwino kuposa munthu wa milomo yopotoka,+ komanso munthu wopusa.+ Miyambo 28:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Munthu wosauka amene akuyenda ndi mtima wosagawanika, ali bwino kuposa munthu aliyense woyenda m’njira zokhota, ngakhale ali wolemera.+ Mlaliki 9:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Mumzindawo munali munthu wina wosauka koma wanzeru, amene anapulumutsa mzindawo chifukwa cha nzeru zake.+ Koma kenako palibe amene anakumbukira munthu wosaukayo.+
19 Wosauka amene akuyenda ndi mtima wosagawanika ali bwino kuposa munthu wa milomo yopotoka,+ komanso munthu wopusa.+
6 Munthu wosauka amene akuyenda ndi mtima wosagawanika, ali bwino kuposa munthu aliyense woyenda m’njira zokhota, ngakhale ali wolemera.+
15 Mumzindawo munali munthu wina wosauka koma wanzeru, amene anapulumutsa mzindawo chifukwa cha nzeru zake.+ Koma kenako palibe amene anakumbukira munthu wosaukayo.+