Miyambo 15:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ndi bwino kukhala ndi zinthu zochepa ukuopa Yehova,+ kusiyana ndi kukhala ndi zinthu zambiri koma uli ndi nkhawa.+ Miyambo 16:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndi bwino kukhala ndi zinthu zochepa mwachilungamo+ kuposa kukhala ndi zinthu zambiri koma mopanda chilungamo.+ Yakobo 2:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Tamverani abale anga okondedwa. Mulungu anasankha anthu amene ali osauka+ m’dzikoli kuti akhale olemera+ m’chikhulupiriro ndi olandira cholowa cha ufumu umene anaulonjeza kwa omukonda,+ sanatero kodi?
16 Ndi bwino kukhala ndi zinthu zochepa ukuopa Yehova,+ kusiyana ndi kukhala ndi zinthu zambiri koma uli ndi nkhawa.+
8 Ndi bwino kukhala ndi zinthu zochepa mwachilungamo+ kuposa kukhala ndi zinthu zambiri koma mopanda chilungamo.+
5 Tamverani abale anga okondedwa. Mulungu anasankha anthu amene ali osauka+ m’dzikoli kuti akhale olemera+ m’chikhulupiriro ndi olandira cholowa cha ufumu umene anaulonjeza kwa omukonda,+ sanatero kodi?