Salimo 37:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Zinthu zochepa za munthu wolungama ndi zabwino+Kusiyana ndi zinthu zochuluka za anthu ambiri oipa.+ Miyambo 15:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ndi bwino kukhala ndi zinthu zochepa ukuopa Yehova,+ kusiyana ndi kukhala ndi zinthu zambiri koma uli ndi nkhawa.+ 1 Timoteyo 6:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndithudi, kukhala wodzipereka kwa Mulungu+ kumeneko limodzi ndi kukhala wokhutira ndi zimene tili nazo,+ ndi njiradi yopezera phindu lalikulu.+
16 Zinthu zochepa za munthu wolungama ndi zabwino+Kusiyana ndi zinthu zochuluka za anthu ambiri oipa.+
16 Ndi bwino kukhala ndi zinthu zochepa ukuopa Yehova,+ kusiyana ndi kukhala ndi zinthu zambiri koma uli ndi nkhawa.+
6 Ndithudi, kukhala wodzipereka kwa Mulungu+ kumeneko limodzi ndi kukhala wokhutira ndi zimene tili nazo,+ ndi njiradi yopezera phindu lalikulu.+