2 Akorinto 4:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 pamene tikuika maso athu pa zinthu zosaoneka, osati pa zooneka.+ Pakuti zooneka n’zakanthawi,+ koma zosaoneka n’zamuyaya.+ Afilipi 1:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Pakuti kwa ine, ndikakhala moyo, ndikhalira moyo Khristu,+ ndipo ndikamwalira+ ndipindula.
18 pamene tikuika maso athu pa zinthu zosaoneka, osati pa zooneka.+ Pakuti zooneka n’zakanthawi,+ koma zosaoneka n’zamuyaya.+