Miyambo 21:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Kupeza chuma pogwiritsa ntchito lilime lonama kuli ngati nkhungu imene imachoka mofulumira.+ Anthu ochita zinthu mwa njira imeneyi akufunafuna imfa.+ Yeremiya 17:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Munthu wopeza chuma mopanda chilungamo+ ali ngati nkhwali imene yasonkhanitsa mazira amene sinaikire. Chuma chakecho adzachisiya asanakwanitse ngakhale hafu ya zaka za moyo wake,+ ndipo pamapeto pake adzaonekera kuti ndi wopusa.”+ Mika 6:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Kodi m’nyumba ya munthu woipa mukupezekabe chuma chopezedwa mopanda chilungamo,+ ndiponso muyezo woperewera wa efa* umene ndi wosaloleka?
6 Kupeza chuma pogwiritsa ntchito lilime lonama kuli ngati nkhungu imene imachoka mofulumira.+ Anthu ochita zinthu mwa njira imeneyi akufunafuna imfa.+
11 Munthu wopeza chuma mopanda chilungamo+ ali ngati nkhwali imene yasonkhanitsa mazira amene sinaikire. Chuma chakecho adzachisiya asanakwanitse ngakhale hafu ya zaka za moyo wake,+ ndipo pamapeto pake adzaonekera kuti ndi wopusa.”+
10 Kodi m’nyumba ya munthu woipa mukupezekabe chuma chopezedwa mopanda chilungamo,+ ndiponso muyezo woperewera wa efa* umene ndi wosaloleka?