Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yoswa 7:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Kenako, ana a Isiraeli anachimwa mwa kuphwanya lamulo lokhudza zinthu zoyenera kuwonongedwa. Anachimwa pamene Akani+ mwana wa Karami, mwana wa Zabidi, mwana wa Zera, wa fuko la Yuda, anatengako zina mwa zinthu zoyenera kuwonongedwa.+ Chifukwa cha zimenezi, Yehova anakwiya kwambiri ndi ana a Isiraeli.+

  • 2 Mafumu 5:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Pamenepo Namani anamuuza kuti: “Chabwino. Tenga matalente awiri.” Anamuumiriza+ mpaka anam’mangira matalente awiri a siliva m’matumba awiri, ndi zovala ziwiri. Anapereka zinthuzo kwa atumiki ake awiri kuti am’nyamulire.

  • Miyambo 10:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Chuma cha anthu oipa chidzakhala chopanda phindu,+ koma chilungamo n’chimene chidzapulumutse munthu ku imfa.+

  • Amosi 3:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Anthuwo sadziwa kuchita zolungama,+ ndipo asonkhanitsa munsanja zawo zokhalamo zinthu zimene anafunkha mwachiwawa,”+ watero Yehova.’

  • Yakobo 5:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Golide ndi siliva wanu wadyedwa ndi dzimbiri, ndipo dzimbiri limenelo lidzakhala umboni wokutsutsani. Lidzadya mnofu wa matupi anu. Zimene mwaunjika+ m’masiku otsiriza+ zili ngati moto.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena