Yoswa 6:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Koma zinthu zoyenera kuwonongedwa musamale nazo,+ kuopera kuti mungazikhumbire+ n’kutengako zinthuzo,+ n’kuchititsa msasa wa Isiraeli nawonso kukhala chinthu choyenera kuwonongedwa ndi kunyanyalidwa.+
18 Koma zinthu zoyenera kuwonongedwa musamale nazo,+ kuopera kuti mungazikhumbire+ n’kutengako zinthuzo,+ n’kuchititsa msasa wa Isiraeli nawonso kukhala chinthu choyenera kuwonongedwa ndi kunyanyalidwa.+