Yoswa 7:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ndiyeno Yoswa anati: “N’chifukwa chiyani wachititsa kuti tinyanyalidwe?+ Iweyo lero Yehova akunyanyala.” Atatero, Aisiraeli onse anawaponya miyala,+ kenako anawatentha ndi moto.+ Choncho, anawaponya miyala. 1 Mbiri 2:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Mwana wa Karami+ anali Akari,* amene anachititsa Isiraeli kunyanyalidwa.+ Iye anachita zinthu zosakhulupirika zokhudzana ndi chinthu choyenera kuwonongedwa.+
25 Ndiyeno Yoswa anati: “N’chifukwa chiyani wachititsa kuti tinyanyalidwe?+ Iweyo lero Yehova akunyanyala.” Atatero, Aisiraeli onse anawaponya miyala,+ kenako anawatentha ndi moto.+ Choncho, anawaponya miyala.
7 Mwana wa Karami+ anali Akari,* amene anachititsa Isiraeli kunyanyalidwa.+ Iye anachita zinthu zosakhulupirika zokhudzana ndi chinthu choyenera kuwonongedwa.+