Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 38:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Patapita miyezi itatu, Yuda anauzidwa kuti: “Tamara mpongozi wako anachita chiwerewere,+ ndipo ali ndi pakati.”+ Yuda atamva zimenezo, anati: “M’tulutseni kuti aphedwe ndi kuotchedwa.”+

  • Levitiko 20:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 “‘Mwamuna akakwatira mkazi n’kugonanso ndi mayi a mkaziyo, limenelo ndi khalidwe lotayirira.+ Aziphedwa ndi kutenthedwa,+ onse mwamunayo ndi akaziwo, kuti khalidwe lotayirira+ lisapitirire pakati panu.

  • Levitiko 21:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 “‘Mwana wamkazi wa wansembe akadziipitsa mwa kuchita uhule, pamenepo waipitsa bambo ake. Aziphedwa ndi kutenthedwa.+

  • Yoswa 7:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Amene apezeke ndi zinthu zoyenera kuwonongedwazo, adzatenthedwa ndi moto,+ iye limodzi ndi banja lake ndi zonse ali nazo. Adzatenthedwa chifukwa waphwanya pangano la Yehova,+ ndiponso wachita cholakwa chochititsa manyazi mu Isiraeli.”’”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena