Levitiko 21:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “‘Mwana wamkazi wa wansembe akadziipitsa mwa kuchita uhule, pamenepo waipitsa bambo ake. Aziphedwa ndi kutenthedwa.+
9 “‘Mwana wamkazi wa wansembe akadziipitsa mwa kuchita uhule, pamenepo waipitsa bambo ake. Aziphedwa ndi kutenthedwa.+