Genesis 38:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Patapita miyezi itatu, Yuda anauzidwa kuti: “Tamara mpongozi wako anachita chiwerewere,+ ndipo ali ndi pakati.”+ Yuda atamva zimenezo, anati: “M’tulutseni kuti aphedwe ndi kuotchedwa.”+ Levitiko 20:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “‘Mwamuna akakwatira mkazi n’kugonanso ndi mayi a mkaziyo, limenelo ndi khalidwe lotayirira.+ Aziphedwa ndi kutenthedwa,+ onse mwamunayo ndi akaziwo, kuti khalidwe lotayirira+ lisapitirire pakati panu.
24 Patapita miyezi itatu, Yuda anauzidwa kuti: “Tamara mpongozi wako anachita chiwerewere,+ ndipo ali ndi pakati.”+ Yuda atamva zimenezo, anati: “M’tulutseni kuti aphedwe ndi kuotchedwa.”+
14 “‘Mwamuna akakwatira mkazi n’kugonanso ndi mayi a mkaziyo, limenelo ndi khalidwe lotayirira.+ Aziphedwa ndi kutenthedwa,+ onse mwamunayo ndi akaziwo, kuti khalidwe lotayirira+ lisapitirire pakati panu.