Yoswa 1:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Munthu aliyense wopandukira malamulo anu,+ ndi wosamvera mawu anu pa chilichonse chimene mungamulamule, ameneyo aphedwe.+ Inuyo mukhale wolimba mtima ndipo muchite zinthu mwamphamvu.”+ Yoswa 7:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ndiyeno Yoswa anati: “N’chifukwa chiyani wachititsa kuti tinyanyalidwe?+ Iweyo lero Yehova akunyanyala.” Atatero, Aisiraeli onse anawaponya miyala,+ kenako anawatentha ndi moto.+ Choncho, anawaponya miyala.
18 Munthu aliyense wopandukira malamulo anu,+ ndi wosamvera mawu anu pa chilichonse chimene mungamulamule, ameneyo aphedwe.+ Inuyo mukhale wolimba mtima ndipo muchite zinthu mwamphamvu.”+
25 Ndiyeno Yoswa anati: “N’chifukwa chiyani wachititsa kuti tinyanyalidwe?+ Iweyo lero Yehova akunyanyala.” Atatero, Aisiraeli onse anawaponya miyala,+ kenako anawatentha ndi moto.+ Choncho, anawaponya miyala.