Yoswa 6:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Koma zinthu zoyenera kuwonongedwa musamale nazo,+ kuopera kuti mungazikhumbire+ n’kutengako zinthuzo,+ n’kuchititsa msasa wa Isiraeli nawonso kukhala chinthu choyenera kuwonongedwa ndi kunyanyalidwa.+ 1 Mbiri 2:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Mwana wa Karami+ anali Akari,* amene anachititsa Isiraeli kunyanyalidwa.+ Iye anachita zinthu zosakhulupirika zokhudzana ndi chinthu choyenera kuwonongedwa.+
18 Koma zinthu zoyenera kuwonongedwa musamale nazo,+ kuopera kuti mungazikhumbire+ n’kutengako zinthuzo,+ n’kuchititsa msasa wa Isiraeli nawonso kukhala chinthu choyenera kuwonongedwa ndi kunyanyalidwa.+
7 Mwana wa Karami+ anali Akari,* amene anachititsa Isiraeli kunyanyalidwa.+ Iye anachita zinthu zosakhulupirika zokhudzana ndi chinthu choyenera kuwonongedwa.+