Yoswa 7:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Aisiraeli achimwa, ndiponso aphwanya pangano+ limene ndinawalamula kuti alisunge. Iwo atenga zina mwa zinthu zoyenera kuwonongedwa.+ Aba+ zinthuzo ndi kuzibisa+ pakati pa katundu wawo.+
11 Aisiraeli achimwa, ndiponso aphwanya pangano+ limene ndinawalamula kuti alisunge. Iwo atenga zina mwa zinthu zoyenera kuwonongedwa.+ Aba+ zinthuzo ndi kuzibisa+ pakati pa katundu wawo.+