Ekisodo 20:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 “Usabe.+ Yesaya 61:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Pakuti ine Yehova ndimakonda chilungamo.+ Ndimadana ndi zauchifwamba ndi kupanda chilungamo.+ Ndidzawapatsa malipiro awo mokhulupirika,+ ndipo ndidzachita nawo pangano lomwe lidzakhalapo mpaka kalekale.+ Mateyu 15:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Mwachitsanzo, maganizo oipa, za kupha anthu, za chigololo, za dama, za kuba, maumboni onama, ndi zonyoza Mulungu,+ zimachokera mumtima.+
8 Pakuti ine Yehova ndimakonda chilungamo.+ Ndimadana ndi zauchifwamba ndi kupanda chilungamo.+ Ndidzawapatsa malipiro awo mokhulupirika,+ ndipo ndidzachita nawo pangano lomwe lidzakhalapo mpaka kalekale.+
19 Mwachitsanzo, maganizo oipa, za kupha anthu, za chigololo, za dama, za kuba, maumboni onama, ndi zonyoza Mulungu,+ zimachokera mumtima.+