Rute 2:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Yehova akudalitse chifukwa cha zimene wachita,+ ndipo Yehova, Mulungu wa Isiraeli akufupe mokwanira.+ Iye amene m’mapiko mwake wathawiramo ndi kupezamo chitetezo.”+ Salimo 117:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pakuti kukoma mtima kosatha kumene watisonyeza ndi kwakukulu.+Ndipo choonadi+ cha Yehova chidzakhalapobe mpaka kalekale.Tamandani Ya, anthu inu!+ Zekariya 8:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndithu ndidzawabweretsa, ndipo adzakhala mu Yerusalemu.+ Iwo adzakhala anthu anga+ ndipo ine ndidzakhala Mulungu wawo woona ndi wachilungamo.’”+
12 Yehova akudalitse chifukwa cha zimene wachita,+ ndipo Yehova, Mulungu wa Isiraeli akufupe mokwanira.+ Iye amene m’mapiko mwake wathawiramo ndi kupezamo chitetezo.”+
2 Pakuti kukoma mtima kosatha kumene watisonyeza ndi kwakukulu.+Ndipo choonadi+ cha Yehova chidzakhalapobe mpaka kalekale.Tamandani Ya, anthu inu!+
8 Ndithu ndidzawabweretsa, ndipo adzakhala mu Yerusalemu.+ Iwo adzakhala anthu anga+ ndipo ine ndidzakhala Mulungu wawo woona ndi wachilungamo.’”+