Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Miyambo 6:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Pali zinthu 6 zimene Yehova amadana nazo.+ Zilipo zinthu 7 zimene moyo wake umanyansidwa nazo:+

  • Yeremiya 7:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Kodi mungamabe,+ kupha,+ kuchita chigololo,+ kulumbira monama,+ kufukiza nsembe zautsi kwa Baala+ ndi kutsatira milungu ina imene simunali kuidziwa,+

  • Zekariya 8:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Musamakonzerane ziwembu mumtima mwanu kuti muonetsane tsoka+ ndipo musamakonde kulumbira monama.+ Pakuti zinthu zonsezi ine ndimadana nazo,’+ watero Yehova.”

  • Malaki 3:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 “Kodi munthu wochokera kufumbi angabere Mulungu? Komatu inu mukundibera.”

      Inu mukunena kuti: “Takuberani motani?”

      “Mukundibera kudzera m’chakhumi* ndi m’zopereka.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena