Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mafumu 18:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Kenako Eliya anayandikira anthu onsewo n’kunena kuti: “Kodi mukayikakayika* mpaka liti?+ Ngati Yehova ali Mulungu woona m’tsateni,+ koma ngati Baala ndiye Mulungu woona tsatirani ameneyo.” Koma anthuwo sanamuyankhe chilichonse.

  • 2 Mafumu 23:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Mfumuyo inachotsa ntchito ansembe a milungu yachilendo, amene mafumu a Yuda anawaika kuti azifukiza nsembe yautsi pamalo okwezeka m’mizinda ya Yuda ndi malo ozungulira Yerusalemu. Inachotsanso ntchito ansembe ofukiza nsembe yautsi kwa Baala,+ kwa dzuwa, kwa mwezi, kwa magulu a nyenyezi, ndi kwa khamu lonse la zinthu zakuthambo.+

  • Yeremiya 11:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Pakuti milungu yako, iwe Yuda,+ yafanana ndi mizinda yako kuchuluka kwake. Ndipo chinthu chochititsa manyazi+ mwachimangira maguwa ansembe, anthu inu. Mwachimangira maguwa ansembe ochuluka mofanana ndi misewu ya mu Yerusalemu. Mwamanga maguwa ansembe kuti muzifukizira Baala nsembe zautsi.’+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena